A7-G
Zinthu Zikuluzikulu Zimene Yesu Anachita Ali Padziko Lapansi—Utumiki Womaliza wa Yesu mu Yerusalemu (Gawo 1)
NTHAWI |
MALO |
ZIMENE ZINACHITIKA |
MATEYU |
MALIKO |
LUKA |
YOHANE |
---|---|---|---|---|---|---|
33, Nisani 8 |
Betaniya |
Yesu anafika ku Betaniya kutatsala masiku 6 kuti Pasika achitike |
||||
Nisani 9 |
Betaniya |
Anamuthira mafuta mʼmutu |
||||
Betaniya-Betefage-Yerusalemu |
Analowa mu Yerusalemu monga wopambana, atakwera bulu |
|||||
Nisani 10 |
Betaniya-Yerusalemu |
Anatemberera mtengo wamkuyu; anayeretsanso kachisi |
||||
Yerusalemu |
Ansembe aakulu ndi alembi anakonza chiwembu kuti aphe Yesu |
|||||
Mawu a Yehova anamveka; Yesu ananeneratu za imfa yake; kusakhulupirira kwa Ayuda kunakwaniritsa ulosi |
||||||
Nisani 11 |
Betaniya-Yerusalemu |
Mtengo wamkuyu umene unafota |
||||
Yerusalemu, mʼkachisi |
Anakayikira ulamuliro wa Khristu; fanizo la ana aamuna awiri |
|||||
Mafanizo: alimi oipa, phwando la ukwati |
||||||
Anayankha mafunso okhudza Mulungu ndi Kaisara, kuuka kwa akufa komanso lamulo lalikulu kuposa onse |
||||||
Anafunsa zokhudza Khristu |
||||||
Anadzudzula alembi ndi Afarisi |
||||||
Mkazi wamasiye anapereka zopereka |
||||||
Phiri la Maolivi |
Chizindikiro cha kukhalapo kwake |
|||||
Mafanizo: anamwali 10, matalente, nkhosa ndi mbuzi |
||||||
Nisani 12 |
Yerusalemu |
Atsogoleri anakonza zopha Yesu |
||||
Yudasi anakonza zopereka Yesu |
||||||
Nisani 13 (Lachinayi masana) |
Pafupi ndi Yerusalemu, ndi mkati mwake Anakonzekera |
Pasika womaliza |
||||
Nisani 14 |
Yerusalemu |
Anadya Pasika limodzi ndi atumwi |
||||
Anasambitsa mapazi a atumwi ake |