Lipoti la Chaka cha Utumiki cha 2023 la Mboni za Yehova Padziko Lonse

Onani zimene a Mboni za Yehova achita pa ntchito yolalikira padziko lonse kuyambira mu September 2022 mpaka August 2023.

Ziwerengero Zonse za 2023

Lipoti lapachakali likusonyeza zimene a Mboni za Yehova achita pa ntchito yawo yolalikira padziko lonse.

Lipoti la Mayiko Komanso Madera la 2023

Mu lipotili, muli chiwerengero cha anthu onse a Mboni, chiwerengero cha amene anabatizidwa, amene anapezeka pa mwambo wa Chikumbutso ndi zina zambiri.

Mwina Mungakondenso Kudziwa Izi

MAFUNSO OFUNSIDWA KAWIRIKAWIRI

Kodi a Mboni za Yehova Alipo Angati Padziko Lonse?

Werengani kuti mudziwe mmene timapezera chiwerengero cha Mboni za Yehova.

MAFUNSO OFUNSIDWA KAWIRIKAWIRI

N’chifukwa Chiyani Mumalalikira Kunyumba ndi Nyumba?

Dziwani zimene Yesu anauza ophunzira ake oyambirira kuti azichita.

Mavidiyo Othandiza Muutumiki

Kodi a Mboni za Yehova ndi Anthu Otani?

Anthu ambiri amafuna atadziwa kuti a Mboni za Yehova ndi anthu otani. Onerani vidiyoyi kuti akuuzeni okha zimene amakhulupirira.

ZOKHUDZA IFEYO

Mboni za Yehova padziko lonse

Werengani kuti mudziwe mmene a Mboni za Yehova alili ogwirizana padziko lonse.

ZOKHUDZA IFEYO

Kodi Phunziro la Baibulo Limachitika Bwanji?

A Mboni za Yehova padziko lonse lapansi amadziwika bwino chifukwa cha ntchito yawo yophunzitsa anthu Baibulo kwaulere. Onani mmene amaphunzitsira.