Zomwe Zili M’bukuli
Zomwe Zili M’bukuli
M’bukuli Muli . . .
MALEMBA
amene akufotokoza mfundo zikuluzikulu
MFUNDO YOTHANDIZA
izi ndi mfundo zokuthandizani kuti zinthu zizikuyenderani bwino
KODI MUKUDZIWA . . .?
zimenezi ndi mfundo zokuthandizani kuganiza
ZOTI NDICHITE
pamenepa muzilembapo zimene mukufuna kuchita pogwiritsa ntchito zimene mwawerenga
KODI INUYO MUKUGANIZA BWANJI?
awa ndi mafunso okuthandizani kunena maganizo anu pa zimene mwawerenga
Komanso Muli . . .
MFUNDO ZANGA
tsamba limeneli likupezeka kumapeto kwa chigawo chilichonse ndipo muzilembapo maganizo anu
CHITSANZO CHABWINO
patsambali pakumakhala nkhani ya munthu wa m’Baibulo woti timutsanzire