Chimwemwe
N’chiyani chikusonyeza kuti Yehova ndi Mulungu wachimwemwe?
Kodi ndi zifukwa ziti zimene zimatichititsa kukhala osangalala?
Sl 100:2; Mla 8:15; Yes 65:14, 18; Afi 4:1, 4
Onaninso Sl 64:10; Yes 61:10; Mt 5:11, 12
Nkhani za m’Baibulo zomwe zingakuthandizeni:
Sl 16:7-9, 11—Wamasalimo Davide anali wosangalala chifukwa chokhala pa ubwenzi wabwino ndi Yehova
Ahe 12:1-3—Mtumwi Paulo anafotokoza kuti nafenso, mofanana ndi Yesu, tikhoza kukhala osangalala ngakhale kuti tili munthawi yovuta chifukwa cha chiyembekezo chomwe tili nacho