Pitani ku nkhani yake # link, for screen reader ##

Pitani ku mitu ya nkhani

Mlozera Nkhani wa Magazini a Galamukani! a 2010

Mlozera Nkhani wa Magazini a Galamukani! a 2010

Mlozera Nkhani wa Magazini a Galamukani! a 2010

CHIPEMBEDZO

Buku Limene Mungathe Kulikhulupirira (Baibulo), 11/10, 12/10

Kodi Khirisimasi Inayamba Bwanji? 12/10

Kodi Ndi Nzeru Kukhulupirira Mulungu? 2/10

Kulambira Njoka, 3/10

Okhulupirira Kuti Kulibe Mulungu, 11/10

MAUNANSI A ANTHU

Kodi Mungakhulupirire Ndani? 10/10

Kudyera Pamodzi, 1/10

Kusungulumwa, 9/10

Kuthetsa Banja, 2/10

Malangizo Otithandiza Kulamulira Lilime, 11/10

“Mwina Nyimbo Ndi Imene Ingathandize,” 9/10

MAYIKO NDI ANTHU

Anthu a ku Thailand, 5/10

Anthu a mtundu wa Batak (Indonesia), 8/10

Anyani Ochititsa Chidwi a ku Indonesia, 7/10

Chakudya Chotentha Kuntchito (India), 11/10

Chivomezi cha ku Haiti, 12/10

Dzina la Mulungu (tchalitchi cha ku Canada), 7/10

Dzuwa Linafiira Ngati Magazi (Iceland), 2/10

Kufufuza Njira Kumpoto kwa Dziko Lapansi, 10/10

Mabwato (Canada), 5/10

Manda a Pansi pa Nthaka a ku Odessa (Ukraine), 3/10

Mfumukazi Elizabeti I (England), 1/10

Mont Blanc, 4/10

Msika wa ku Africa, 1/10

Mtedza Wokoma wa ku Australia, 11/10

Njanji Yochoka Kunyanja Kukafikanso Kunyanja (Canada), 6/10

Nkhalango ya Amazon, 4/10

Nyumba Zoyenda Nazo za Anthu a ku Asia, 9/10

“Wotchi Yaikulu Kwambiri Padziko Lonse” (Britain), 10/10

Zilumba za Faeroe, 3/10

MBIRI YA MOYO WA ANTHU

Loya Anafufuza Zimene Mboni za Yehova Zimaphunzitsa (L. Civin), 8/10

Mulungu Wanditonthoza (V. Colloy), 12/10

Ndikungoona Kuchedwa Kudzawauza Kuti, “Tonse Tilipo” (A. Austin), 8/10

Ndinakopeka ndi Mboni za Yehova (T. Orosco), 3/10

“Ndinakulira M’banja Losakhulupirira Kuti Kuli Mulungu” (F. Vyskočil), 11/10

Ndinali Msilikali Panopa Ndikutumikira Mulungu (G. Bernhardt), 2/10

Ndinalowa Mpikisano Wabwino Kwambiri (K. Bergman), 9/10

Ndinasankha Ntchito Yabwino (P. Kostadinov), 4/10

Ndinasiya Ntchito ya Ndalama Zambiri (M. Márquez), 6/10

Ngakhale Ndinalumala, Ndine Wosangalalabe (J. Várguez), 5/10

MBONI ZA YEHOVA

Aphunzitsi Amachita Chidwi (Bulgaria), 9/10

‘Buku Lothandiza Kwambiri’ (Mphunzitsi Waluso), 7/10

Chivomezi cha ku Haiti, 12/10

Dzina la Mulungu Likulengezedwabe, 7/10

Galamukani! Inathandiza Mayi Kuti Asachotse Mimba, 2/10

Kabuku Kothandiza Ophunzira Baibulo (‘Onani Dziko Lokoma’), 10/10

“Kuphunzira Baibulo Kukuthandiza Anthu Osamva,” 7/10

‘Kuthetsa Mtima Wodzikonda’ (Gibraltar), 1/10

‘Lekani Kuda Nkhawa’ (India), 1/10

Mayi Wina Ali ndi Ufulu Wolera Ana Ake (Spain), 7/10

Misonkhano Yachigawo ya “Khalanibe pa Ubwenzi ndi Yehova,” 5/10, 6/10

Mukufuna Kukhala Bwenzi la Mulungu? (Mexico), 1/10

Mumadziwa Zotani za Mboni za Yehova? 8/10

“Ndikupempha Kuti Mundithandize” (kabuku ka Munthu Amene Mumakonda Akamwalira), 2/10

“Simunataye Mtima” (mayi wa mwana wolumala), 11/10

NYAMA NDI ZOMERA

Anyani, 4/10

Anyani Ochititsa Chidwi, 7/10

Chakudya cha Tizilombo, 3/10

Chimtengo Chochokera ku Kanthanga, 9/10

Diso la Kadziwotche, 7/10

Diso la Nkhanu, 11/10

Kankhono Kam’madzi, 9/10

Khungu la Shaki, 2/10

Lilime la Mbalame ya Choso, 10/10

Mahatchi Ofatsa, 8/10

Mapiko a Tombolombo, 8/10

Mbalame Zampala, 6/10

‘Mbalame Zouluka Mogometsa,’ 7/10

Mbira Zam’mapiri, 10/10

Mfumu ya Nkhalango, 9/10

Mleme Waung’ono Kwambiri, 2/10

Mlomo wa Nankapakapa, 4/10

Mtedza wa Makadamiya, 11/10

Nankapakapa (mbalame), 2/10

Nsomba za Salimoni, 12/10

Ulimi wa Maluwa, 1/10

Ziphaniphani, 6/10

SAYANSI

Anakwanitsa Zinthu Zimene Zinali Zosatheka, 5/10

Himogulobini, 9/10

Kugunda kwa Mtima, 5/10

Pali Umboni Wasayansi Wotsimikizira Zoti Kulibe Mulungu? 11/10

Panagona Luso! 1/10, 2/10, 4/10, 6/10, 7/10, 8/10

9/10, 10/10, 11/10, 12/10

Zinalipo Kale M’chilengedwe, 3/10

UMOYO NDI MANKHWALA

Chimfine, 6/10

Chipatala Choyendayenda, 3/10

Matenda Amene Anavuta Kwambiri (kolera), 10/10

Matenda Ofooketsa Mafupa, 6/10

Matenda Otupa Chiwindi, 8/10

Mungatani Mutadwala Pokwera Phiri? 7/10

Munthu Angatani Kuti Asiye Kusuta? 5/10

Muzinyadira Khungu Lanu, 5/10

Zimene Mungachite Ngati Mumapanikizika Kwambiri, 6/10

ZACHUMA NDI NTCHITO

Chakudya Chotentha Kuntchito, 11/10

Mumapanikizika ndi Ntchito? 1/10

Ngati Ntchito Yatha Mungasamale Bwanji Ndalama? 7/10

ZIMENE ACHINYAMATA AMADZIFUNSA

Kodi N’kulakwa Kuchita Zinthu Zina Pandekha? 3/10

Kugonana Tili Pachibwenzi Kungachititse Kuti Tizikondana Kwambiri? 4/10

N’chifukwa Chiyani Anyamata Sandifunsira? 1/10

N’chifukwa Chiyani Ndimangokhalira Kukangana Ndi Makolo Anga? 2/10

N’chifukwa Chiyani Ndiyenera Kusamalira Thanzi Langa? 6/10

Ndingakwanitse Bwanji Zolinga Zanga? 10/10

Ndingakwanitse Kukakhala Pandekha? 7/10

Ndingatani Kuti Ndisamadziderere? 5/10

Ndingatani Kuti Ndisamangokhala Wokhumudwa? 9/10

Ndingatani Kuti Ndizigwirizana Ndi Abale Anga? 8/10

Ndisiye Sukulu? 11/10

Zimene Baibulo Limanena pa Nkhani Yogonana Amuna Kapena Akazi Okhaokha, 12/10

ZIMENE BAIBULO LIMANENA

Bwanji Mulungu Osangomuwononga Mdyerekezi? 12/10

Kodi Akazi Ayenera Kukhala Atumiki Mumpingo? 7/10

Kodi Atsogoleri Achipembedzo Ayenera Kulipidwa? 6/10

Kodi Mbali Zonse za Baibulo N’zothandiza? 3/10

Kodi Mulungu Ndi Mphamvu Chabe? 10/10

Kodi Tiyenera Kupemphera kwa “Oyera”? 11/10

Kodi Ziwanda N’zotani? 8/10

Kugwiritsa Ntchito Ndalama Mwanzeru, 5/10

Kutembenuzira Munthu Tsaya Lina, 9/10

N’chiyani Chimachititsa Munthu Kukhala Wabwino Kapena Woipa? 4/10

Tsiku Lachiweruzo, 1/10

Zoyenera Kuchita Mukakhala Pachibwenzi, 2/10

ZOSIYANASIYANA

Chibwibwi, 5/10

Fupa Ndi Lolimba Modabwitsa, 1/10

Kodi Gasi Amachokera Kuti? 11/10

Kodi Nthawi Imakucheperani? 4/10

Mawu Amene Amagwiritsa Ntchito Zikawavuta Panyanja, 10/10

Tiyembekezere Zivomezi Zinanso Zikuluzikulu, 12/10