GALAMUKANI! Na. 3 2020 | Kodi Tsankho Lidzatha?
Kuti tigonjetse mtima watsankho tiyenera kusintha maganizo athu komanso mmene timaonera zinthu. Werengani magaziniyi kuti muone njira 5 zomwe zingatithandize kuthetsa mtima watsankho.
Kodi Muli Ndi Mtima Watsankho?
Kodi ndi zinthu ziti zomwe zingasonyeze kuti ndife atsankho?
Muzidziwa Zoona Zake
Ngati sitidziwa zolondola, tikhoza kumaona anthu ena molakwika. Onani mmene zinthu zomwe zinachitikira munthu wina yemwe poyamba anali msilikali zikusonyezera mfundo imeneyi.
Muzimvera Ena Chisoni
Kodi kusamvera ena chisoni kumasonyeza chiyani?
Muzizindikira Kuti Ena Amakuposani
Kudzikonda kungachititse kuti munthu akhale watsankho. Koma kodi n’chiyani chomwe chingatithandize kuti tisakhale ndi mtima umenewu?
Muzicheza Ndi Anthu Osiyanasiyana
Onani ubwino wocheza ndi anthu omwe mumasiyana nawo zinthu zina.
Muzisonyeza Chikondi
Chikondi chingatithandize kuthetsa mtima watsankho. Onani zina mwa njira zomwe chikondi chingatithandizire kuchotsa mtima watsankho.
Tsankho Lidzatha
Kodi ndi zinthu 4 ziti zomwe Ufumu wa Mulungu udzachite pothetsa tsankho?
Anasiya Tsankho
Onerani mavidiyo atatu omwe akusonyeza anthu ena omwe anakwanitsa kusiya tsankho.