NSANJA YA OLONDA (YOPHUNZIRA) August 2024
M’magaziniyi muli nkhani zophunzira kuyambira October 7–November 10, 2024.
NKHANI YOPHUNZIRA 31
Zimene Yehova Wachita Kuti Atipulumutse ku Uchimo ndi Imfa
Idzaphunziridwa mlungu wa October 7-13, 2024.
Mafunso Ochokera kwa Owerenga
Kodi mawu akuti kuika chizindikiro a pa 2 Atesalonika 3:14, akunena zimene mpingo uyenera kuchita, kapena zimene Mkhristu aliyense payekha ayenera kuchita?
NKHANI YOPHUNZIRA 32
Yehova Amafuna Kuti Anthu Onse Alape
Idzaphunziridwa mlungu wa October 14-20, 2024.
NKHANI YOPHUNZIRA 33
Kodi Mpingo Ungatsanzire Bwanji Maganizo a Yehova pa Nkhani ya Anthu Ochimwa?
Idzaphunziridwa mlungu wa October 21-27, 2024.
NKHANI YOPHUNZIRA 34
Mmene Tingasonyezere Chikondi ndi Chifundo Wina Akachita Tchimo
Idzaphunziridwa mlungu wa October 28–November 3, 2024.
NKHANI YOPHUNZIRA 35
Kodi Akulu Angathandize Bwanji Anthu Amene Achotsedwa Mumpingo?
Idzaphunziridwa mlungu wa November 4-10, 2024.
Mawu kwa Owerenga
M’magaziniyi muli nkhani zophunzira zimene zikufotokoza mmene Yehova amaonera anthu amene achimwa komanso mmene amawathandizira. Zikufotokozanso zimene tingachite potsanzira chifundo komanso chikondi cha Yehova.