NSANJA YA OLONDA September 2015 | Kodi a Mboni za Yehova Ndi Anthu Otani?
Kuti mudziwe zolondola ponena za Mboni za Yehova, mungachite bwino kuwafunsa eni akewo.
NKHANI YAPACHIKUTO
Kodi a Mboni za Yehova Mumawadziwa Bwinobwino?
Kodi inuyo mumaona a Mboni ngati mmene anthu ena omwe atchulidwa m’nkhaniyi amaganizira?
NKHANI YAPACHIKUTO
Kodi a Mboni za Yehova Amakhulupirira Zotani?
Kukhulupira kuti Baibulo ndi Mawu a Mulungu kumakhudza zonse zimene timachita.
NKHANI YAPACHIKUTO
Kodi Timapeza Bwanji Ndalama Zoyendetsera Ntchito Yathu?
Kodi timapeza bwanji ndalama? Nanga timazigwiritsa ntchito bwanji?
NKHANI YAPACHIKUTO
N’chifukwa Chiyani Timalalikira?
Pali zifukwa zitatu zikuluzikulu zomwe zimatichititsa kuti tizilalikira.
MBIRI YA MOYO WANGA
Ndinapeza Chinthu Chamtengo Wapatali Kuposa Kukhala Wotchuka
Mina Hung Godenzi anakhala munthu wotchuka kwambiri. Koma sankakhala mosangalala ngati mmene ankaganizira poyamba.
Baibulo la Bedell Linathandiza Kuti Anthu Ayambe Kumvetsa Mawu a Mulungu
Baibulo limeneli lakhala likugwiritsidwa ntchito kwa zaka 300.
Kodi Nthawi Zina Mumaimba Mulungu Mlandu?
Kodi munayamba mwafunsapo kuti, ‘N’chifukwa chiyani Mulungu analola kuti zimenezi zindichitikire?’
Kuyankha Mafunso a M’Baibulo
Kodi maulosi a m’Baibulo amatithandiza bwanji?
Zina zimene zili pawebusaiti
Kodi Nkhondo ya Aramagedo Idzakhala Yotani?
Mawu akuti Aramagedo amapezeka kamodzi kokha m’Baibulo, koma nkhondo imene mawuwa amatanthauza imatchulidwa m’Baibulo lonse.