Pitani ku nkhani yake # link, for screen reader ##

TIMABUKU TOTHANDIZA ANTHU KUTIDZIWA BWINO PADZIKO LONSE

A Mboni za Yehova Komanso Nkhani ya Kusalowerera Ndale

A Mboni za Yehova Komanso Nkhani ya Kusalowerera Ndale

Mogwirizana ndi zimene Baibulo limaphunzitsa, a Mboni za Yehova sachita nawo zandale. Maboma ambiri amaona kuti zimenezi zimalimbikitsa mtendere ndipo amavomereza kuti a Mboni ndi anthu omvera malamulo komanso amalemekeza ndiponso kuchita zinthu mogwirizana ndi akuluakulu a boma.