Mboni za Yehova Padziko Lonse

Romania

  • Bucharest, Romania​—Akuuza anthu uthenga wa m’Baibulo

Mfundo Zachidule—Romania

  • 18,944,000—Chiwerengero cha anthu
  • 39,723—Chiwerengero cha Mboni za Yehova
  • 528—Mipingo
  • Pa anthu 480 alionse pali wa Mboni za Yehova m’modzi

NSANJA YA OLONDA (YOPHUNZIRA)

Bambo Anga Anamwalira Koma Ndinapeza Bambo Ena

Werengani mbiri ya moyo wa M’bale Gerrit Lösch, wa m’Bungwe Lolamulira.