Mboni za Yehova Padziko Lonse

United States of America

  • Dyer Bay, Maine, United States—Akuphunzitsa pogwiritsa ntchito Baibulo

  • Dera la Tallahassee ku Florida m’dziko la United States​—Akumuonetsa vidiyo yakuti Kodi pa Nyumba ya Ufumu Pamachitika Zotani?

Mfundo Zachidule—United States of America

  • 336,679,000—Chiwerengero cha anthu
  • 1,233,609—Chiwerengero cha Mboni za Yehova
  • 11,942—Mipingo
  • Pa anthu 276 alionse pali wa Mboni za Yehova m’modzi

ZOCHITIKA PA MOYO

Mfundo Zothandiza Anthu Ogwira Ntchito Zachipatala Omwe Ali Ndi Nkhawa

Kodi manesi Komanso ogwira ntchito pachipatala china anapeza bwanji mfundo zolimbikitsa pa nthawi ya mliri wa COVID-?

MOYO WA PA BETELI

Tikukuitanani Kuti Mudzaone Maofesi Athu ku United States

Mudzaonanso Likulu la Padziko Lonse la Mboni za Yehova lomwe lili ku United States.

NSANJA YA OLONDA (YOPHUNZIRA)

Anadzipereka ndi Mtima Wonse ku New York

N’chiyani chinachititsa anthu okhala m’nyumba yabwino kwambiri kuti alolere kusamukira m’kanyumba kakang’ono kwambiri