Ntchito Zomangamanga
NTCHITO ZOMANGAMANGA
Kugwira Ntchito ndi a Mboni za Yehova
Tamvani mmene zimakhalira pogwira ntchito yomanga nyumba zikuluzikulu ndi a Mboni za Yehova.
NTCHITO ZOMANGAMANGA
Kugwira Ntchito ndi a Mboni za Yehova
Tamvani mmene zimakhalira pogwira ntchito yomanga nyumba zikuluzikulu ndi a Mboni za Yehova.
Zithunzi Zosonyeza Ntchito Yomanga ku Britain—Gawo 7 (Kuyambira mu September 2018 Mpaka mu February 2019)
Onani mmene ntchito yamanga ofesi ya nthambi yatsopano ya Mboni za Yehova inayendera ku Chelmsford m’dziko la Britain.
Zithunzi Zosonyeza Ntchito Yomanga ku Britain—Gawo 6 (Kuyambira March Mpaka August 2018)
Onani zithunzi zatsopano zosonyeza mmene ntchitoyi ikuyendera.
Zithunzi Zosonyeza Ntchito Yomanga ku Britain—Gawo 4 (Kuyambira March Mpaka August 2017)
Ntchito yomanga maofesi atsopano ndi nyumba zogona ili mkati ku Britain.
A Mboni Akuteteza Zachilengedwe Mumzinda wa Chelmsford
A Mboni za Yehova ku Britain ayamba kumanga ofesi yawo yanthambi yatsopano pafupi ndi mzinda wa Chelmsford. Kodi akuchitapo chiyani kuti ateteze zachilengedwe?
Zithunzi Zosonyeza Ntchito Yomanga ku Philippines Gawo 2 (Kuyambira June 2015 Mpaka June 2016)
Posachedwapa, a Mboni za Yehova ku Philippines anamaliza ntchito yaikulu yokonza nyumba za ofesi ya nthambi mumzinda wa Quezon. Onani mmene ntchitoyi inayendera.
A Mboni za Yehova Akumanga Nyumba za Ufumu Zambiri
Kuyambira mu 1999, a Mboni za Yehova amanga Nyumba za Ufumu zoposa 5,000 ku Mexico ndiponso mayiko ena 7 a ku Central America. N’chifukwa chiyani anthu ena omwe si a Mboni amafunitsitsa Nyumba za Ufumu zitamangidwa m’dera lawo?
Anzathu Atsopano ku Warwick
Akuluakulu a tawuni ya Warwick ndi enanso akufotokoza zinthu zabwino zimene zakhala zikuchitika pamene ankagwira ntchito ndi a Mboni za Yehova pomanga likulu lawo latsopano.
“Akazi Angathe Kugwira Nawo Ntchito ya Zomangamanga”
Mungadabwe kudziwa ntchito zimene akazi akugwira.
Zithunzi Zosonyeza Ntchito Yomanga ku Warwick Gawo 6 (Kuyambira March Mpaka August 2016)
Miyezi yomaliza kugwira ntchito yomanga likulu latsopano lapadziko lonse la Mboni za Yehova ku Warwick, New York.
Anthu Omwe si Mboni Anasangalala Kugwira Ntchito Ndi Mboni za Yehova ku Warwick
Kodi ogwira ntchito komanso madalaivala omwe si a Mboni ananena zotani atagwira ntchito ndi a Mboni pa ntchito yomanga?
Ochititsa Lendi Nyumba Analembera a Mboni za Yehova Makalata
Kodi anthu ena anafotokoza zotani atachititsa lendi nyumba zawo kwa a Mboni za Yehova?
Zithunzi Zosonyeza Ntchito Yomanga ku Warwick Gawo 5 (Kuyambira September 2015 Mpaka February 2016)
Ntchito imene inalipo kunja ndi mkati mwa nyumba yomwe muli maofesi inaphatikizapo kuika nyale zoti usiku ziziwalitsa chizindikiro cha Watch Tower, denga loonekera mkati, matailosi a konkire komanso kanjira kokhala ndi denga.
Zithunzi za Ntchito Yomanga ku Warwick—Gawo 2 (Kuyambira September Mpaka December 2014)
Ntchito yomanga likulu latsopano la Mboni za Yehova ikuyenda bwino. Pa nthawi ina, mashini okwezera zinthu m’mwamba okwana 13 ankagwira ntchito nthawi imodzi.
Zithunzi za Ntchito Yomanga ku Warwick—Gawo 3 (Kuyambira January Mpaka April 2015)
Pofika mu February, anthu okwana 2,500 ankagwira nawo ntchitoyi tsiku lililonse ndipo anthu pafupifupi 500 obwera kudzagwira ntchito pa kanthawi ankafika mlungu uliwonse. Onani zithunzizi kuti muone mmene ntchitoyi ikuyendera.
Zithunzi za Ntchito Yomanga ku Warwick—Gawo 4 (Kuyambira May Mpaka August 2015)
Makoma ndi madenga anaikidwa panyumba ina yogona ndipo njira zodutsa anthu popita kunyumba zina zinaikidwa. Anayambanso ntchito yodzala kapinga, maluwa ndi mitengo.
Zithunzi za Ntchito Yomanga ku Britain—Gawo 1 (Kuyambira January Mpaka August 2015)
Onani mmene ntchito yomanga ofesi ya nthambi ikuyendera ku Britain pafupi ndi mzinda wa Chelmsford, m’dera la Essex.
Zithunzi za Ntchito Yomanga ku Philippines—Gawo 1 (Kuyambira February 2014 Mpaka May 2015)
A Mboni za Yehova akumanga nyumba zatsopano ndi kukonzanso zina zakale ku ofesi ya ku Philippines imene ili mumzinda wa Quezon.
Zithunzi Zosonyeza Ntchito Yomanga ku Wallkill Gawo 1 (Kuyambira July 2013 Mpaka October 2014)
Onani mmene ntchito yowonjezera maofesi a Mboni za Yehova ku Wallkill munzinda wa New York, U.S.A. ikuyendera
Zithunzi Zosonyeza Ntchito Yomanga ku Warwick Gawo 1 (Kuyambira May Mpaka August 2014)
Onani mmene ntchito yomanga galaja, maofesi komanso nyumba yogona C ndi D ikuyendera.
A Mboni za Yehova ku Nigeria Amanga Nyumba za Ufumu Zokwana 3,000
A Mboni za Yehova ku Nigeria anachita msonkhanowu pokumbukira kuti m’dzikoli mwamangidwa Nyumba za Ufumu 3,000. Pa mwambowu panafotokozedwa mbiri yachidule yokhudza ntchito ya a Mboni za Yehova m’dzikoli kuyambira m’ma 1920.
M’nkhalango ya Amazon Munamangidwa Nyumba Yochitira Misonkhano
A Mboni ena amayenda paboti kwa masiku atatu kuti akachite msonkhano ku Nyumba Yochitira Misonkhanoyi.
Mmene ntchito yomanga ikuyendera ku Warwick #2
Antchito ongodzipereka ochokera m’mayiko osiyanasiyana akumangira limodzi malo omwe adzakhale likulu la padziko lonse la Mboni za Yehova
Ntchito Yomanga Nyumba za Ufumu M’madera a Kumidzi
Onani mmene magulu okwana 5 a anthu ongodzipereka ankagwirira ntchito kuti amange Nyumba za Ufumu ziwiri m’masiku 28 okha.
Kusamutsa Likulu la Padziko Lonse Ndi Mbiri Yosaiwalika
A Mboni za Yehova akumanga likulu lawo latsopano ku Warwick m’dera la New York. Iwo akukhulupirira kuti Mulungu akuwatsogolera pa ntchitoyi.
Kuteteza Zachilengedwe ku Warwick
A Mboni za Yehova ayamba ntchito yomanga maofesi omwe akhale likulu lawo latsopano la padziko lonse ku New York. Kodi iwo akuchita zotani pofuna kuteteza zachilengedwe?
Nyumba za Ufumu Zakwana 1,000 Ndipo Zina Zikumangidwabe
A Mboni za Yehova ku Philippines amanga Nyumba za Ufumu zoposa 1,000.
Mmene Ntchito Yomanga Ikuyendera ku Warwick #1
Ntchito ikuyenda bwino ku Warwick, m’dera la New York, pamalo amene adzakhale likulu la Mboni za Yehova padziko lonse. Tamvani zimene anthu ena a Mboni amene anadzipereka n’kugwira nawo ntchitoyi anena zokhudza ntchitoyi.
Anthu Ongodzipereka Akugwira Ntchito Yotamandika ku Tuxedo
Anthu a Mboni za Yehova ochokera ku United States ndi m’mayiko ena akudzipereka n’kumagwira nawo ntchito yomanga ku Tuxedo, m’dera la New York. N’chifukwa chiyani akuchita zimenezi?
Amapempha Kuti Agwire Ntchito Koma Safuna Kulipidwa
Kwa zaka zoposa 28 zapitazi, a Mboni za Yehova amanga nyumba zosiyanasiyana m’mayiko oposa 120, ndipo amagwira ntchitoyi mongodzipereka. Werengani nkhaniyi kuti mudziwe zambiri zokhudza ntchito imeneyi.
Ntchito Yomanga Ikuyenda Bwino Kwambiri ku Wallkill ndi ku Warwick
Ntchito yaikulu yomanga nyumba ndi maofesi atsopano a Mboni za Yehova ku United States ikuyenda bwino kwambiri. Ntchitoyi ikuchitika m’malo awiri ndipo anthu ongodzipereka, ochokera m’dziko lomweli, ndi amene akugwira ntchitoyi.
Mkulu Waboma Wochokera ku Ofesi Yoona za Zopewa Ngozi Anayamikira a Mboni
Ku Australia, a Mboni za Yehova anayamikiridwa chifukwa choyesetsa kwambiri kutsatira malangizo opewera ngozi pa ntchito yawo yomanga Nyumba ya Ufumu.
A Mboni za Yehova Akufuna Kusamutsa Likulu Lawo la Padziko Lonse
N’chifukwa chiyani tikusamutsira likulu lathu la padziko lonse kumpoto kwa New York pambuyo pokhala ku Brooklyn kuyambira m’chaka cha 1909?