Turkmenistan
A Mboni za Yehova ku Turkmenistan
● A Mboni Anamangidwa Chifukwa cha Chikhulupiriro Chawo—???
Dziko la Turkmenistan Likukana Kupereka Ufulu Wotsatira Zimene Munthu Amakhulupirira
A Mboni awiri anaweruzidwa kuti akakhale m’ndende chifukwa chokana usilikali. Dziko la Turkmenistan likukanabe kupereka ufulu wokana usilikali chifukwa cha zimene munthu amakhulupirira ndipo sililola kuti anthu azigwira ntchito ina m’malo mwa usilikali.
Kodi a Bahram Hemdemov Amasulidwa Nawo Ulendo Ukubwerawu?
A Mboni za Yehova akuyembekezera kuti pa ulendo wotsatira wotulutsa anthu m’ndende, mtsogoleri wa dziko la Turkmenistan a Gurbanguly Berdimuhamedov adzatulutsanso a Hemdemov.
Ikusonyeza 1 - 15 ya 19