Pitani ku nkhani yake # link, for screen reader ##

Mayankho a Zimene Achinyamata Amafunsa, Buku Lachiwiri

Mayankho a Zimene Achinyamata Amafunsa, Buku Lachiwiri

Mukufunikira malangizo odalirika. Mungawapeze m’buku lakuti Mayankho a Zimene Achinyamata Amafunsa, Buku Lachiwiri. M’bukuli muli ndemanga zochokera kwa achinyamata ambiri apadziko lonse omwe tinawafunsa. Malangizo anzeru a m’Baibulo anawathandiza. Mudzaona kuti angakuthandizeninso inuyo.

Bukuli lingakuthandizeni kuyankha mafunso okhudza:

  • Kusirira Mnyamata Kapena Mtsikana

  • Kusintha kwa Thupi

  • Anzanu

  • Moyo wa Kusukulu

  • Nkhani Zokhudza Ndalama

  • Makolo Anu

  • Mtima Wanu

  • Zosangalatsa

  • Kukula Mwauzimu

Mukhoza kupanga dawunilodi bukuli kapena mungalembere maofesi athu kuti mupemphe buku losindikizidwa.

Dziwani izi: Tsopano ndi zotheka kulemba mawu pa PDF ya buku limeneli. Ngati chipangizo chanu chili ndi pulogalamu yotere, mukhoza kulemba mayankho komanso ndemanga zanu m’buku limeneli.