ZOTI MUCHITE Kodi Nthawi Zina Mumasowa Mpata Wochitira Zinthu Panokha? YAMBANI Zimene mungachite kuti anthu ena azikudalirani kwambiri. Pangani Dawunilodi Nkhani Zina Zoti Achinyamata Achite Achinyamata Mwina Mungakondenso Kudziwa Izi ZIMENE ACHINYAMATA AMAFUNSA Kodi Ndingatani Kuti Ndizikhala ndi Mpata Womachita Zinthu Pandekha? Kodi mumaona kuti makolo anu akukulondalondani? Nanga mungatani kuti vuto limeneli lichepe? MAVIDIYO AMAKATUNI Kodi Ndingatani Kuti Makolo Anga Azindilolako Kuchita Zinthu Zina? Mukhoza kuganiza kuti makolo anu akuyenera kumakuonani kuti ndinu munthu wamkulu, koma iwo sangagwirizane ndi maganizo amenewa. Kodi mungachite zinthu ziti kuti makolo anu ayambe kukukhulupirirani? ZIMENE ACHINYAMATA AMAFUNSA N’chifukwa Chiyani Ndiyenera Kukhala Mwamtendere ndi Abale Anga? Ngakhale kuti mumakonda abale anu, koma nthawi zina mukhoza kuwakhumudwitsa. ZIMENE ACHINYAMATA AMAFUNSA Kodi Ndingatani Kuti Makolo Anga Azindikhulupirira? Kuphunzira kukhala wodalirika ndi kofunika kwa aliyense osati kwa achinyamata okha. Patsani ena Patsani ena Kodi Nthawi Zina Mumasowa Mpata Wochitira Zinthu Panokha? ZOTI ACHINYAMATA ACHITE Kodi Nthawi Zina Mumasowa Mpata Wochitira Zinthu Panokha? Chichewa Kodi Nthawi Zina Mumasowa Mpata Wochitira Zinthu Panokha? https://cms-imgp.jw-cdn.org/img/p/502016259/univ/art/502016259_univ_sqr_xl.jpg