Pulogilamu ya Msonkhano Wacigawo wa 2022
Tsiku Loyamba
Pulogilamu ya tsiku loyamba yazikidwa pa Salimo 29:11—“Yehova adzadalitsa anthu ake ndi mtendele.”
Tsiku Laciŵili
Pulogilamu ya tsiku lociŵili yazikidwa pa 2 Petulo 3:14—“Adzakupezeni opanda banga, opanda cilema ndiponso muli mu mtendele.”
Tsiku Lacitatu
Pulogilamu ya tsiku lacitatu yazikidwa pa Aroma 15:13—“Mulungu amene amapeleka ciyembekezo akudzazeni ndi cimwemwe conse ndi mtendele wonse.”
Mawu kwa Osonkhana
Mawu othandiza kwa opezeka pa msonkhano wacigawo.