Pulogilamu ya Msonkhano wa Cigawo wa 2024 wakuti “Lengezani Uthenga Wabwino!”

Tsiku Loyamba

Pulogilamu ya tsiku loyamba yazikika pa Luka 2:10​—“Uthenga wabwino wa cimwemwe cacikulu cimene anthu onse adzakhale naco.”

Tsiku Laciŵili

Pulogilamu ya tsiku laciŵili yazikika pa Salimo 96:2​—“Tsiku ndi tsiku muzilengeza uthenga wabwino wa cipulumutso cake.”

Tsiku Lacitatu

Pulogilamu ya pa tsiku lothela yazikika pa Mateyu 24:14​—“. . . kenako mapeto adzafika.”

Mawu kwa Osonkhana

Mawu othandiza opezeka pa msonkhano wa cigawo.

Mungakondenso Izi

ZOKHUDZA IFE MBONI

Kapezekemponi pa Msonkhano wa Cigawo wa 2024 wakuti​—Lengezani Uthenga Wabwino!

Tikuitanilani kuti mukapezeke ku msonkhano wa cigawo wa Mboni za Yehova wa masiku atatu.

MISONKHANO IKULUIKULU

Tikukuitanilani ku Msonkhano wa Cigawo wa Mboni za Yehova wa 2024 wakuti “Lengezani Uthenga Wabwino!”

Tikukuitanilani ku msonkhano wa cigawo wa masiku atatu wa Mboni za Yehova.