Onani zimene zilipo

Onani nkhani zake

GALAMUKA! Na. 3 2018 | Thandizo Kwa Ofedwa

Kodi tingapeze kuti thandizo kuti tipilile cisoni tikafedwa?

Nkhani za m’magazini ino, zidzafotokoza zimene mungayembekezele ngati munthu amene mumam’konda wamwalila, komanso zimene mungacite kuti mupilile cisoni.

 

Kuŵaŵa kwa Imfa

Imfa ya mnzako wa m’cikwati, m’bululu wako, kapena mnzako wapamtima, ni imodzi mwa zinthu zovutitsa kwambili maganizo komanso zoŵaŵitsa mtima. Onani zimene akatswili komanso ofedwa amakamba.

Zimene Mungayembekezele

Kodi ni mavuto anji amene wofedwa amayembekezela munthu amene amam’konda akamwalila?

Zimene Mungacite Palipano Mukafedwa

Ambili amene anataikilidwa okondedwa awo, apeza citonthozo mwa kuseŵenzetsa njila zothandiza.

Thandizo Lodalilika Kwambili kwa Ofedwa

Baibo ingapeleke thandizo lodalilika kwambili kwa ofedwa.

M’magazini Ino: Thandizo Kwa Ofedwa

Magazini ino ya Galamuka! ipeleka thandizo kwa ofedwa.