NSANJA YA MLONDA May 2015 | Kodi Mungakonde Kuphunzila Baibulo?

Anthu mamiliyoni padziko lonse akupindula ndi pulogalamu yaulele yophunzila Baibulo ndi Mboni za Yehova. Inunso mungapindule ndi maphunzilo amenewa.

NKHANI YA PACIKUTO

N’cifukwa Ciani Muyenela Kuphunzila Baibulo?

Kodi mumakamba kuti, ‘Ndine wotangwanika,’ kapena kuti, ‘Ndimacita mantha kuyamba kuphunzila Baibulo’?

Pulogalamu Yophunzila Baibulo ya Anthu Onse

Pezani mayankho a mafunso 8 amene amafunsidwa kaŵilikaŵili okhudza pulogalamu yathu yophunzitsila Baibulo.

NKHANI YA PACIKUTO

Cifukwa Cake Tifunika Kupulumutsidwa

Kodi zingakhale zomveka kuti Mulungu wacikondi atipatse mtima wofuna kukhala ndi moyo mpaka kalekale, koma n’kulephela kuukwanilitsa?

NKHANI YA PACIKUTO

Imfa ndi Kuukitsidwa kwa Yesu—Kodi Zili ndi Tanthauzo Lotani kwa Inu?

Mfundo 6 za m’Baibulo zofotokoza mmene imfa ya munthu mmodzi ingacititsile anthu ambili kupeza moyo.

NKHANI YA PACIKUTO

Kukumbukila Imfa ya Yesu—Liti ndipo Kuti?

Mu 2015, Cikumbutso ca Imfa ya Yesu Cidzacitika pa Cisanu April 3, dzuwa litaloŵa.

MBILI YANGA

Jairo Amagwilitsila Nchito Maso Ake Potumikila Mulungu

Ngakhale kuti Jairo akuvutika ndi matenda ovuta kwambili a muubongo akusangalalabe.

Kuyankha Mafunso A m’Baibulo

Pa mwambo wokumbukila imfa ya Yesu, ndani ayenela kudya mkate ndi kumwa vinyo?