Phunzilani kwa Mabwenzi a Yehova
Phunzilani kwa anthu osiyanasiyana ochulidwa m’Baibulo amene anakhala mabwenzi a Yehova!
Abele
Kodi mungaphunzile ciyani kwa Abele pa nkhani yolimbitsa cikhulupililo canu mwa Yehova?
Yeremiya
Kodi mungaphunzile ciyani kwa Yeremiya amene anali bwenzi la Yehova pa nkhani ya kukhala wolimba mtima?
Hananiya, Misayeli, ndi Azariya
Kodi mungakhale omvela monga mabwenzi a Yehova awa, Hananiya, Misayeli, ndi Azariya?
Pepani, palibe mawu olingana amene mwasankha.