Kwa Yehova, Ndise Amodzi
Daunilodi:
1. Mavuto m’dzikoli, kuzondana
Kulikonse kulibe mtendele.
Anthu avutana si okondwa.
Ise tidalila dzina ya M’lungu.
(MWANA WA KOLASI)
Titsatila mawu ake
Sitili mbali ya dziko.
(KOLASI)
Ise mu zocita zathu zonse
Timaonetsa cikondi.
Ndipo tikonde abale athu.
Tisiyana koma kwa Yehova
Ndise’amodzi.
Amodzi.
Amodzi.
2. Inde kulikonse tingayende
Nako kuli anthu a Yehova
Olo tide nkhawa timadziŵa—
Tidzakhala m’dziko la mtendele.
(MWANA WA KOLASI)
Tidalila mawu ake
Sitili mbali ya dziko.
(KOLASI)
Ise mu zocita zathu zonse
Timaonetsa cikondi,
Ndipo tikonde abale athu.
Tisiyana koma kwa Yehova
Ndise’amodzi.
Amodzi.
(MWANA WA KOLASI)
Tiyeni tipililebe
Sitili mbali ya dziko.
(KOLASI)
Ise mu zocita zathu zonse
Timaonetsa cikondi.
Ndipo tikonde abale athu
Tisiyana koma kuli Yehova.
(KOLASI)
Ise mu zocita zathu zonse
Timaonetsa cikondi,
Ndipo tikonde abale athu.
Tisiyana koma kwa Yehova
Ndise’amodzi
Amodzi
Amodzi
Amodzi.
Amodzi.
Amodzi.